This snapshot, taken on 03/08/2004, shows web content selected for preservation by The National Archives. External links, forms and search boxes may not work in archived websites.

Report on reading in English in primary schools in Zambia - Education Research Paper No. 05, 1993, 55 p.

[Previous Page] [Table of Contents] [Next Page]

Appendix F - Nyanja reading test: Extracts

V.01

Dzina.............................. Tsiku lobadwa.............................
Kalasi............................. Mwamuna/mkazi........................
Sukulu............................ Chilakulo canu............................

Ndime Yophunzirira

Mpira

ng'ombe

amakonda

wofiyira

ndipo

ndi

mpira

Ana atatu ali kusewela ndi mpira ________. Siwa ali kuponyera ________ kwa Simon. Iye awungwira ________ kuponyera kwa Maria. Onse ________ kusewela ndi mpira.

Atate ace a Mumbi

amawathandiza

m'mawa

matimati

onse

kudimba

galu

Atate ace a Mumbi ndi mlimi. Ali ndi dimba lalikulu. Liri pafupi ndi mudzi wawo. Matsiku onse amauka ________ ndi kuyenda ________ kwao. Amalima nyemba, ________ mdi cimanga cabiri. Mumbi ________ kudimba.

Miriamu

amayenda

atate

amakonda

Sayenda

iye


wamkazi

kanyumba

Iwo

Amakhala

Miriam ali ndi zaka khumi. Ali ndi mung'ono wace wamwamuna ndi wamkazi. ________ mu ________ kakang'ono ndi amai ndi ________ awo. Matsiku onse Miriam ndi mung'ono wace wamwamuna ________ kusukulu. Mung'ono wace ________ Jelita ali ndi zaka ziwiri. kusukulu.

Atate ace a Sifo

madzi

aphunzitsi

mauzu

woyera

Iwo

sayena

mitengo

zitatu

Mbuzi


Atae ace a Sifo ali ndi ng'ombe ________ ndi mbuzi zisanu ndi ziwiri. Ng'ombe ndi ________ za mawanga akuda ndi. ________ ndi zakatondo. Simadya ________ ndi kumwa akumsinje. Tsiku loweruka, pamene Sifo ________ ku sukulu, amaziyang'anira.

Mabvuto ndi njinga yace

iye

imodzi

munjira

kukuwa

suga

kuyenda

Mabvuto akuyendetsa njinga yace ________. Ali ________ ku sitoro kukagula ________. Pali galu pabwalo mwa ________ ya nyumbazo.

kukuwira

galu

imayamba

munjira

basiketi

pansi

Ngati yawona Mabvuto ________ kumuthamangitsa. Basiketi ya mabvuto yagwa ________. Mzimai atuluka mnyumba ndi ________ galu. Ndipo atenga ________ ndikumupatsa Mabvuto.

[Previous Page] [Top of Page] [Next Page]